Tsiku lililonse msonkhano wachigawo ukatha, muzidzadina linki ya tsiku limenelo kuti mudzaone kapena kupanga dawunilodi zinthu zomwe zatulutsidwa patsikulo.