Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Zimene Tinganene

Zimene Tinganene

●○○ ULENDO WOYAMBA

Funso: Kodi Mulungu amawaona bwanji anthu amene amamufunafuna ndi mtima wonse?

Lemba: 1 Pet. 5:6, 7

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi Mulungu amaganizira munthu aliyense payekha?

○●○ ULENDO WOBWEREZA WOYAMBA

Funso: Kodi Mulungu amaganizira munthu aliyense payekha?

Lemba: Mat. 10:29-31

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi tikudziwa bwanji kuti Mulungu amatimvetsa?

○○● ULENDO WOBWEREZA WACHIWIRI

Funso: Kodi tikudziwa bwanji kuti Mulungu amatimvetsa?

Lemba: Sal. 139:1, 2, 4

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi kudziwa kuti Mulungu amatikonda n’kothandiza bwanji?