Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AHEBERI 9-10

‘Chithunzi cha Zinthu Zabwino Zimene Zikubwera’

‘Chithunzi cha Zinthu Zabwino Zimene Zikubwera’

9:12-14, 24-26; 10:1-4

Chihema chinkaimira zimene Mulungu anakonza zoti adzakhululukire anthu machimo awo onse pogwiritsa ntchito nsembe ya Yesu. Gwirizanitsani zinthu 4 za pachihema ndi zimene zinkaimira.

  1. Nsalu yotchinga

  2. Kuwaza magazi a nyama patsogolo pa guwa la nsembe

  3. Malo Oyera Koposa

  4. Mkulu wa ansembe

 
  • Yesu

  • Kumwamba

  • Kukapereka mtengo wa nsembe yake kwa Yehova

  • Thupi la Khristu