Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

September 9-​15

AHEBERI 9-10

September 9-​15

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Chithunzi cha Zinthu Zabwino Zimene Zikubwera”: (10 min.)

  • Aheb. 9:12-14​—Magazi a Khristu ndi apamwamba kwambiri kuposa a mbuzi komanso a ng’ombe (it-1 862 ¶1)

  • Aheb. 9:24-26​—Khristu anakapereka mtengo wa nsembe yake kwa Mulungu ndipo anachita zimenezi kamodzi kokha (cf 183 ¶4)

  • Aheb. 10:1-4​—Chilamulo chinkaimira zinthu zabwino zimene zikubwera m’tsogolo (it-2 602-603)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Aheb. 9:16, 17​—Kodi mavesiwa akutanthauza chiyani? (w92 3/1 31 ¶4-6)

  • Aheb. 10:5-7​—Kodi ndi liti pamene Yesu analankhula mawu amenewa, nanga ankatanthauza chiyani? (it-1 249-250)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Aheb. 9:1-14 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 89

 • Kodi Timayamikira Misonkhano Yathu? (Sal. 27:11): (12 min.) Onerani vidiyoyi. Kenako kambiranani mafunso otsatirawa:

  • Kodi ndi zinthu ziti zomwe Yesu, yemwe ndi Mkulu wa Ansembe, akutichitira masiku ano?

  • Kodi tingasonyeze kuyamikira m’njira zitatu ziti?

 • Muzimvetsera Pamisonkhano: (3 min.) Onerani vidiyoyi. Kenako pemphani ana kuti afotokoze chifukwa chake ayenera kumamvetsera akakhala pamisonkhano.

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 50

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 128 ndi Pemphero