Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

September 23-​29

AHEBERI 12-13

September 23-​29

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Chilango Chimasonyeza Kuti Yehova Amatikonda”: (10 min.)

  • Aheb. 12:5​—Mukapatsidwa chilango, musamakhumudwe n’kusiya kuchita zoyenera (w12 3/15 29 ¶18)

  • Aheb. 12:6, 7​—Yehova amalanga anthu amene amawakonda (w12 7/1 21 ¶3)

  • Aheb. 12:11​—Ngakhale kuti chilango ndi chowawa, chimatithandiza kuti tikhale anthu abwino (w18.03 32 ¶18)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Aheb. 12:1​—Kodi chitsanzo cha ‘mtambo waukulu wa mboni’ chimatilimbikitsa bwanji? (w11 9/15 17-18 ¶11)

  • Aheb. 13:9​—Kodi vesili limatanthauza chiyani? (w89 12/15 22 ¶10)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Aheb. 12:1-17 (th phunziro 11)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 115

 • Tizikhalabe Okhulupirika . . . Ngakhale Kuti si Ife Angwiro: (5 min.) Onerani vidiyoyi. Kenako kambiranani mafunso otsatirawa:

  • Kodi M’bale Cázares wakhala akulimbana ndi vuto lotani kungochokera pamene anayamba kutumikira Yehova?

  • Kodi m’baleyu anathandizidwa bwanji?

 • Zofunika Pampingo: (10 min.)

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 52

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 93 ndi Pemphero