Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AHEBERI 7-8

“Wansembe Mpaka Muyaya Monga mwa Unsembe wa Melekizedeki”

“Wansembe Mpaka Muyaya Monga mwa Unsembe wa Melekizedeki”

7:1-3, 17

N’chifukwa chiyani tinganene kuti Melekizedeki ankaimira Yesu?

  • 7:1​—Anali mfumu komanso wansembe

  • 7:3, 22-25​—Palibe pomwe pamasonyeza kuti analowa m’malo kapenanso kulowedwa m’malo ndi munthu wina

  • 7:5, 6, 14-17​—Anachita kusankhidwa kuti akhale wansembe, osati chifukwa chobadwira m’banja la ansembe

Kodi unsembe wa Khristu umaposa bwanji wa Aroni? (it-1 1113 ¶4-5)