CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Chozizwitsa Choyamba cha Yesu”: (10 min.)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Yoh. 1:1​—Kodi n’chiyani chikusonyeza kuti Yohane sankatanthauza kuti “Mawu” anali Mulungu Wamphamvuyonse? (“Mawu” “ndi” “Mawuyo anali mulungu” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 1:1, nwtsty)

  • Yoh. 1:29​—N’chifukwa chiyani Yohane M’batizi anatchula Yesu kuti “Mwanawankhosa wa Mulungu”? (“Mwanawankhosa wa Mulungu” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 1:29, nwtsty)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yoh. 1:1-18

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 38

 • Zofunika Pampingo: (8 min.)

 • Zimene Gulu Lathu Lachita: (7 min.) Onetsani vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya September.

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 3

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 141 ndi Pemphero