Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

September 11-17

Ezekieli 46-48

September 11-17
 • Nyimbo Na. 134 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Aisiraeli Omwe Anachoka ku Ukapolo Analandira Madalitso”: (10 min.)

  • Ezek. 47:1, 7-12​—M’dziko lobwezeretsedwalo anthu anali ndi zokolola zambiri (w99 3/1 10 ¶11-12)

  • Ezek. 47:13, 14​—Banja lililonse linalandira cholowa chake (w99 3/1 10 ¶10)

  • Ezek. 48:9, 10​—Malo asanagawidwe kwa anthu, anaika padera gawo lina la malowo monga “chopereka” kwa Yehova

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Ezek. 47:1, 8; 48:30, 32-34​—N’chifukwa chiyani Ayuda amene anachokera ku ukapolo sankafunika kuona kukwaniritsidwa kwa mbali iliyonse ya masomphenya a Ezekieli onena za kachisi? (w99 3/1 11 ¶14)

  • Ezek. 47:6​—N’chifukwa chiyani Ezekieli akutchulidwa kuti ndi “mwana wa munthu”? (it-2 1001)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Ezek. 48:13-22

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) wp17.5 chikuto​—Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) wp17.5​—Sonyezani mmene mungapangire ulendo wobwereza pogwiritsa ntchito magazini imene munamusiyira pa ulendo woyamba. Kenako musonyezeni limodzi mwa mabuku amene timagwiritsa ntchito pophunzira Baibulo.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 35 ¶17​—Muitanireni kumisonkhano.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 28

 • Zofunika Pampingo: (8 min.) Mukhoza kukambirana zimene tikuphunzira mu Buku Lapachaka. (yb17 64-65)

 • Zimene Gulu Lathu Lachita: (7 min.) Onetsani vidiyo yakuti Zimene Gulu Lathu Lachita ya September.

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 6 ¶16-24, komanso tsamba 67

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 11 ndi Pemphero