Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  September 2017

September 25–October 1

DANIELI 4-6

September 25–October 1
 • Nyimbo Na. 67 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Kodi Mupitiriza kutumikira Yehova Mosalekeza?”: (10 min.)

  • Dan. 6:7-10​—Danieli anaika moyo wake pangozi n’cholinga choti atumikire Yehova mosalekeza (w10 11/15 6 ¶16; w06 11/1 24 ¶12)

  • Dan. 6:16, 20​—Mfumu Dariyo inazindikira kuti Danieli anali pa ubwenzi wolimba ndi Yehova (w03 9/15 15 ¶2)

  • Dan. 6:22, 23​—Yehova anadalitsa Danieli chifukwa chomulambira molimba mtima (w10 2/15 18 ¶15)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Dan. 4:10, 11, 20-22​—Kodi mtengo waukulu womwe Nebukadinezara analota unkaimira chiyani? (w07 9/1 18 ¶5)

  • Dan. 5:17, 29​—N’chifukwa chiyani poyamba Danieli anakana mphatso kuchokera kwa mfumu Belisazara koma pambuyo pake n’kulandira? (w88 10/1 30 ¶3-5; dp 109 ¶22)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Dan. 4:29-37

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) inv

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) inv​—Sonyezani mmene mungapangire ulendo wobwereza pogwiritsa ntchito kapepala koitanira anthu kumisonkhano kamene munagawira pa ulendo woyamba.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 120 ¶16​—Limbikitsani wophunzira kuti azikhalabe wokhulupirika ngakhale pamene achibale ake akumutsutsa.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU