Onerani vidiyo yakuti Muzikhala Okhulupirika Ngati mmene Yesu Analili​—Pamene Mukuyesedwa (imapezeka pamene palembedwa kuti BAIBULO), kenako yankhani mafunso otsatirawa:

  • Kodi Segi anakumana ndi mayesero otani amene akanamuchititsa kuti asakhale wokhulupirika kwa Mulungu?

  • Kodi n’chiyani chinathandiza Segi kuti akhalebe wokhulupirika?

  • Kodi kukhulupirika kwake kunathandiza bwanji kuti Yehova alemekezedwe?