Onerani vidiyo yakuti Muzitsatira Mokhulupirika Mfundo za Yehova​—Muzipewa Kuchita Zinthu ndi Anthu Ochotsedwa (imapezeka pamene palembedwa kuti BAIBULO), kenako yankhani mafunso otsatirawa:

  • Kodi makolo a Sonia anakumana ndi vuto lotani lomwe likanachititsa kuti asakhale okhulupirika kwa Mulungu?

  • Kodi n’chiyani chinawathandiza kuti akhalebe okhulupirika?

  • Kodi kukhulupirika kwawo kwa Yehova kunathandiza bwanji Sonia?