• Nyimbo Na. 131 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Kukhala Okhulupirika kwa Yehova Kumabweretsa Madalitso”: (10 min.)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Dan. 1:5, 8​—N’chifukwa chiyani Danieli ndi anzake atatu aja ankaona kuti adetsedwa akadya zakudya zabwino zochokera kwa mfumu? (it-2 382)

  • Dan. 2:44​—N’chifukwa chiyani Ufumu wa Mulungu udzaphwanye maufumu a padziko lapansi omwe ndi mbali zosiyanasiyana za chifaniziro chomwe Nebukadinezara analota? (w12 6/15 17, bokosi; w01 10/15 6 ¶4)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Dan. 2:31-43

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Yes. 40:22​—Kuphunzitsa Choonadi​—Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Aroma 15:4​—Kuphunzitsa Choonadi​—Musiyireni khadi lodziwitsa anthu za JW.ORG.

 • Nkhani: (Osapitirira 6 min.) w17.02 29-30​—Mutu: Kodi Yehova Amayamba Waganizira Kaye Zimene Tingapirire Ndiyeno N’kusankha Mayesero Oti Tikumane Nawo?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU