Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  September 2016

September 26–October 2

MASALIMO 142-150

September 26–October 2
 • Nyimbo Na. 134 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Yehova ndi Wamkulu ndi Woyenera Kutamandidwa Kwambiri”: (10 min.)

  • Sal. 145:1-9—Ukulu wa Yehova ndi wosasanthulika (w04 1/15 10 ndime 3-4; 11 ndime 7-8; 14 ndime 20-21; 15 ndime 2)

  • Sal. 145:10-13—Atumiki a Yehova okhulupirika amayesetsa kumutamada (w04 1/15 16 ndime 3-6)

  • Sal. 145:14-16—Yehova amafunitsitsa kuthandiza atumiki ake (w04 1/15 17-18 ndime 10-14)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Sal. 143:8—Kodi lembali lingatithandize bwanji kuti tizilemekeza Yehova tsiku lililonse? (w10 1/15 21 ndime 1-2)

  • Sal. 150:6—Kodi lemba lomaliza la m’buku la Masalimo limatsindika mfundo yotani? (w13 11/15 4 ndime 4; it-2-E 448)

  • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Sal. 145:1-21

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) 1 Pet. 5:7—Kuphunzitsa Choonadi.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Sal. 37:9-11—Kuphunzitsa Choonadi.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) fg phunziro 9 ndime 3—Thandizani wophunzira wanu kuti azigwiritsa ntchito zimene waphunzira.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU