Masalimo 120 mpaka 134 amadziwikanso kuti nyimbo zokwerera kumzinda. Anthu ena amakhulupirira kuti Masalimowa ankaimbidwa ndi anthu amene ankapita ku Yerusalemu kukalambira Mulungu. Amakhulupirira kuti anthuwa ankadutsa m’mapiri a ku Yuda akamapita ku zikondwerero za pachaka.

Masalimowa amayerekezera chitetezo cha Yehova ndi . . .

121:3-8

  • M’busa amene ali maso

  • Mthunzi

  • Msilikali wokhulupirika