Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

September 12-18

Masalimo 120-134

September 12-18
 • Nyimbo Na. 33 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Thandizo Langa Lichokera kwa Yehova”: (10 min.)

  • Sal. 121:1, 2—Popeza Yehova analenga zonse, tiyenera kumamukhulupirira kwambiri (w04 12/15 12 ndime 3)

  • Sal. 121:3, 4—Yehova amakhala tcheru nthawi zonse kuti aone zimene atumiki ake akufunikira (w04 12/15 13 ndime 4)

  • Sal. 121:5-8—Yehova ndi wokhulupirika ndipo amateteza anthu ake (w04 12/15 13 ndime 5-7)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Sal. 123:2—Kodi fanizo la “maso a atumiki,” kapena kuti akapolo, lili ndi mfundo yotani? (w06 9/1 15 ndime 4)

  • Sal. 133:1-3—Kodi mavesi amenewa akutiphunzitsa chiyani? (w06 9/1 16 ndime 3)

  • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Sal. 127:1–129:8

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) wp16.5 tsamba loyamba—Kukambirana ndi mwini nyumba yemwe wakwiya.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) wp16.5 tsamba loyamba—Muitanireni kumisonkhano yathu.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) fg phunziro 8 ndime 6—Thandizani wophunzira wanu kuti azigwiritsa ntchito zimene waphunzira.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 114

 • Yehova Wandichitira Zazikulu: (15 min.) Onerani vidiyo ya pa jw.org. Yehova Wandichitira Zazikulu. (Pitani pamene palembedwa kuti ZOKHUDZA IFEYO > ZIMENE TIMACHITA.) Kenako kambiranani mafunso awa: Kodi Yehova anathandiza bwanji Crystal ndipo zimenezi zamulimbikitsa bwanji? Kodi amachita chiyani akayamba kuganizira zinthu zoipa zimene zinamuchitikira? Kodi mwaphunzira chiyani pa zimene zinachitikira Crystal?

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 6 ndime 15-23, bokosi patsamba 57 ndi Mfundo Zofunika Kuganizira patsamba 58

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 119 ndi Pemphero