15:19, 21; 16:33

  • Yesu anagonjetsa dziko popewa kuchita zinthu za m’dzikoli

  • Otsatira a Yesu amayenera kuchita zinthu molimba mtima kuti asasokonezeke ndi maganizo komanso zochita za anthu a m’dzikoli

  • Kutengera chitsanzo cha Yesu yemwe anagonjetsa dziko kungatithandize kuti tizichita zinthu molimba mtima