CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Ndakupatsani Chitsanzo”: (10 min.)

  • Yoh. 13:5​—Yesu anasambitsa mapazi a ophunzira ake (“kusambitsa mapazi a ophunzira” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 13:5, nwtsty)

  • Yoh. 13:12-14​—Ophunzirawo ankayenera “kusambitsana mapazi” (“muyenera” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 13:14, nwtsty)

  • Yoh. 13:15​—Otsatira onse a Yesu ayenera kutengera chitsanzo chake pa nkhani ya kudzichepetsa (w99 3/1 31 ¶1)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Yoh. 14:6​—Kodi Yesu ndi “njira, choonadi ndi moyo” m’njira yotani? (“Ine ndine njira, choonadi ndi moyo” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 14:6, nwtsty)

  • Yoh. 14:12​—Kodi anthu amene amakhulupirira Yesu amachita bwanji “ntchito zazikulu” kuposa zimene iye anachita? (“ntchito zazikulu kuposa zimenezi” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 14:12, nwtsty)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yoh. 13:1-17

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU