Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

October 9-15

DANIELI 10-12

October 9-15
 • Nyimbo Na. 31 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Yehova Ananeneratu Zokhudza Mafumu a Mtsogolo”: (10 min.)

  • Dan. 11:2​—Mafumu 4 analamulira mu ufumu wa Perisiya (dp 212-213 ¶5-6)

  • Dan. 11:3​—Alekizanda Wamkulu anaonekera (dp 213 ¶8)

  • Dan. 11:4​—Ufumu wa Alekizanda unagawanika n’kukhala maufumu 4 (dp 214 ¶11)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Dan. 12:3​—Kodi “anthu ozindikira” ndi ndani, nanga ndi liti pamene “adzawala ngati kuwala kwa kuthambo”? (w13 7/15 13 ¶16, mawu akumapeto)

  • Dan. 12:13​—Kodi Yehova anamulonjeza chiyani Danieli? (dp 315 ¶18)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Dan. 11:28-39

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) g17.5 chikuto​—Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) g17.5 chikuto​—Pitirizani kukambirana zokhudza magazini imene munamupatsa kale. Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Nkhani: (Osapitirira 6 min.) w16.11 5-6 ¶7-8​—Mutu: Kodi Tingatsanzire Bwanji Chitsanzo cha Yehova pa Nkhani Yolimbikitsa Ena?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 113

 • Timalimbikitsidwa ndi Maulosi a M’Baibulo: (15 min.) Onetsani vidiyo yakuti Mawu a Ulosi’ Amatilimbikitsa.

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 8 ¶8-13, komanso tsamba 83

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 126 ndi Pemphero