Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  October 2017

 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | HOSEYA 8-14

Muzipereka Zinthu Zabwino Kwambiri kwa Yehova

Muzipereka Zinthu Zabwino Kwambiri kwa Yehova

14:2, 4, 9

Yehova amasangalala ndi nsembe zathu zabwino ndipo amatidalitsa

TIKAKHALA PA UBWENZI NDI YEHOVA

  1. Timapereka kwa Yehova nsembe zathu zomutamanda

  2. Yehova amatikhululukira, amatikonda komanso timakhala naye pa ubwenzi

  3. Timayamikira madalitso amene timapeza chifukwa chomvera malamulo a Yehova ndipo izi zimatithandiza kuti tizifunitsitsa kumutumikirabe

Kodi ndingatani kuti ndizipereka kwa Yehova zinthu zabwino kwambiri?