Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

October 23-29

HOSEYA 8-14

October 23-29

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Muzipereka Zinthu Zabwino Kwambiri kwa Yehova”: (10 min.)

  • Hos. 14:2​—Yehova amayamikira kwambiri nsembe zimene timamupatsa zomwe ndi “mawu apakamwa pathu” (w07 4/1 20 ¶2)

  • Hos. 14:4​—Yehova amakonda anthu amene amachita zonse zomwe angathe pomutumikira, amawakhululukira machimo, komanso amawaona ngati anzake (w11 2/15 16 ¶15)

  • Hos. 14:9​—Tikamayenda m’njira za Yehova timapindula kwambiri (jd 87 ¶11)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Hos. 10:12​—Kodi tiyenera kuchita chiyani kuti ‘tikolole zipatso za kukoma mtima kosatha’ kwa Yehova? (w05 11/15 28 ¶7)

  • Hos. 11:1​—Kodi mawu a mu vesili anakwaniritsidwa bwanji pa Yesu? (w11 8/15 10 ¶10)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Hos. 8:1-14

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) T-35

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) T-35​—Pitirizani kukambirana zokhudza kapepala kamene munamupatsa pa ulendo woyamba. Sonyezani mmene tingayankhire ngati mwininyumba akutsutsa mfundo inayake.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) lv 152 ¶13-14—Sonyezani mmene tingafikire pamtima wophunzira wathu.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU