Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | DANIELI 7-9

Ulosi wa Danieli Unaneneratu Nthawi Imene Mesiya Adzafike

Ulosi wa Danieli Unaneneratu Nthawi Imene Mesiya Adzafike
ONANI
Kukula kwa Zilembo
Chithunzi

9:24-27

“MILUNGU 70” (ZAKA 490)

 • “MILUNGU 7” (ZAKA 49)

  455 B.C.E. “Mawu . . . onena kuti Yerusalemu akonzedwe”

  406 B.C.E. Yerusalemu anamangidwanso

 • “MILUNGU 62” (ZAKA 434)

 • “MLUNGU UMODZI” (ZAKA 7)

  29 C.E. Mesiya anafika

  33 C.E. Mesiya ‘anaphedwa’

  36 C.E. Mapeto a “milungu 70”