Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  October 2017

October 16-22

HOSEYA 1-7

October 16-22
 • Nyimbo Na. 18 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Kodi Mumasangalala ndi Chikondi Chokhulupirika Ngati Mmene Yehova Amachitira?”: (10 min.)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Hos. 1:7​—Kodi ndi liti pamene Yehova anachitira chifundo ndiponso kupulumutsa nyumba ya Yuda? (w07 9/15 14 ¶7)

  • Hos. 2:18​—Kodi vesili linakwaniritsidwa bwanji m’mbuyomu nanga lidzakwaniritsidwa bwanji mtsogolo? (w05 11/15 20 ¶16; g05 9/8 12 ¶2)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Hos. 7:1-16

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) 1 Yoh. 5:3​—Kuphunzitsa Choonadi​—Muitanireni munthuyo kumisonkhano.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Deut. 30:11-14; Yes. 48:17, 18​—Kuphunzitsa Choonadi​—Mufotokozereni za webusaiti yathu ya jw.org. (Onani mwb16.08 8 ¶2.)

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) lv 12-13 ¶16-18​—Sonyezani mmene tingafikire pamtima wophunzira wathu.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU