Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

October 31–November 6

MIYAMBO 22-26

October 31–November 6
 • Nyimbo Na. 88 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Phunzitsa Mwana M’njira Yomuyenerera(10 min.)

  • Miy. 22:6; 23:24, 25—Makolo akamaphunzitsa ana pogwiritsa ntchito mfundo za m’Baibulo, nthawi zambiri anawo akakula amakhala osangalala ndiponso odalirika (w08 4/1 16; w07 6/1 31)

  • Miy. 22:15; 23:13, 14—M’lembali, “ndodo” imaimira kuphunzitsa, kulangiza komanso kupereka chilango (w15 11/15 5 ndime 6; w07 2/15 27 ndime 18; w97 10/15 32; it-2-E 818 ndime 4)

  • Miy. 23:22—Ngakhale Ana atakula, akhoza kupindula ndi nzeru za makolo awo (w04 6/15 14 ndime 1-3; w00 6/15 21 ndime 13)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza (8 min.)

  • Miy. 24:16—Kodi lembali limatilimbikitsa bwanji kuti tizipirira pa mpikisano wokalandira moyo wosatha? (w13 3/15 4-5 ndime 5-8)

  • Miy. 24:27—Kodi lembali lili ndi mfundo yotani? (w09 10/15 12 ndime 1)

  • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Miy. 22:1-21

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Khadi lodziwitsa anthu za JW.ORG—Kulalikira mwamwayi.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Khadi lodziwitsa anthu za JW.ORG—Muuzeni nkhani imene mudzakambirane mukadzabweranso. Pomaliza, muuzeni kuti mukufuna kumuonetsa vidiyo yakuti N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo?

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) lv 179-181 ndime 18-19

MOYO WATHU WACHIKHRISTU