• Nyimbo Na. 76 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Yesetsani Kukhala Mwamtendere ndi Ena”: (10 min.)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Miy. 17:5—Fotokozani chifukwa chimodzi chimene tiyenera kusankhira zosangalatsa mwanzeru. (w10 11/15 6 ndime 17; w10 11/15 31 ndime 15)

  • Miy. 20:25—Kodi mfundo ya pa lembali ingathandize bwanji anthu amene akufuna kukhala pa chibwenzi komanso kulowa m’banja? (w09 5/15 15-16 ndime 12-13)

  • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Miy. 18:14-24; 19:1-10

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) M’patseni munthuyo kapepala koitanira anthu kumisonkhano. (inv)

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) inv—Pomaliza, muuzeni kuti mukufuna kumuonetsa vidiyo yakuti, Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani?

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) lv 57 ndime 14-15—Thandizani munthuyo kuona kuti ayenera kusintha mmene amavalira akamapita kumisonkhano.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU