• Nyimbo Na. 69 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Nzeru Ndi Yabwino Kuposa Golide”: (10 min.)

  • Miy. 16:16, 17—Munthu wanzeru amaphunzira Mawu a Mulungu komanso kuwagwiritsa ntchito (w07 7/15 8)

  • Miy. 16:18, 19—Munthu wanzeru amapewa kunyada ndiponso kudzikuza (w07 7/15 8-9)

  • Miy. 16:20-24—Munthu wanzeru amalankhula zinthu zothandiza ena (w07 7/15 9-10)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Miy. 15:15—Kodi tingatani kuti tizisangalala kwambiri pa moyo wathu? (11/13 16)

  • Miy. 16:4—Kodi Yehova angagwiritse ntchito bwanji anthu oipa kuti akwaniritse zolinga zake? (w07 5/15 18-19)

  • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Miy. 15:18-33; 16:1-6

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Yoh. 11:11-14—Kuphunzitsa Choonadi. Muitanireni munthuyo kumisonkhano yathu.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Gen. 3:1-6; Aroma 5:12—Kuphunzitsa Choonadi. Muitanireni munthuyo kumisonkhano yathu.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 202 ndime 18-19—Muitanireni munthuyo kumisonkhano yathu.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU