Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  November 2017

November 13-19

OBADIYA 1–YONA 4

November 13-19
 • Nyimbo Na. 42 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Muziphunzirapo Kanthu pa Zimene Munalakwitsa”: (10 min.)

  • [Onetsani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Obadiya.]

  • [Onetsani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Yona.]

  • Yona 3:1-3​—Yona anaphunzirapo kanthu pa zimene analakwitsa (ia 114 ¶22-23)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Obad. 10​—Kodi mawu akuti Edomu ‘sadzakhalaponso mpaka kalekale’ anakwaniritsidwa bwanji? (w07 11/1 13 ¶5)

  • Obad. 12​—Kodi tikuphunzirapo chiyani pa zimene Mulungu ananena podzudzula Aedomu? (jd 112 ¶4-5)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yona 3:1-10

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) wp17.6 chikuto​—Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) wp17.6 chikuto​—Pitirizani kukambirana zokhudza magazini imene munamupatsa kale. Musonyezeni limodzi mwa mabuku amene timagwiritsa ntchito pophunzira Baibulo.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) ld 12-13​—Sankhani zithunzi zoti mukambirane.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU