Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

November 6-12

AMOSI 1-9

November 6-12

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Yesetsani Kufunafuna Yehova Kuti Mupitirize Kukhala ndi Moyo”: (10 min.)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Amosi 2:12​—Kodi tingagwiritse ntchito bwanji mfundo zimene tikuphunzira muvesili? (w07 10/1 14 ¶8)

  • Amosi 8:1, 2​—Kodi “dengu la zipatso za m’chilimwe” linkasonyeza chiyani? (w07 10/1 14 ¶6)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Amosi 4:1-13

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Kukonzekera Ulaliki wa Mwezi Uno: (15 min.) Kukambirana “Zitsanzo za Ulaliki.” Pambuyo poonetsa vidiyo ya chitsanzo cha ulaliki iliyonse, kambiranani mfundo zikuluzikulu za m’vidiyoyo.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU