Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  November 2017

 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MIKA 1-7

Kodi Yehova Amafuna Kuti Tizichita Chiyani?

Kodi Yehova Amafuna Kuti Tizichita Chiyani?

6:6-8

Yehova amatidziwa bwino kwambiri ndipo sayembekezera kuti tizichita zomwe sitingathe. Iye amaona kuti kugwirizana ndi Akhristu anzathu n’kofunika kwambiri pa kulambira kwathu. Ngati tikufuna kuti Yehova azilandira nsembe zathu tiyenera kukonda abale athu komanso kuwalemekeza.