• Nyimbo Na. 26 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Kodi Yehova Amafuna Kuti Tizichita Chiyani?”: (10 min.)

  • [Onetsani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Mika.]

  • Mika 6:6, 7​—Nsembe zimene timapereka kwa Yehova zimakhala zopanda phindu ngati timalephera kuchitira anzathu zinthu zabwino (w08 5/15 6 ¶20)

  • Mika 6:8​—Zimene Yehova amafuna kuti tizichita n’zoti tikhoza kukwanitsa (w12 11/1 22 ¶4-7)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Mika 2:12​—Kodi ulosi umenewu unakwaniritsidwa bwanji? (w07 11/1 15 ¶5)

  • Mika 7:7​—N’chifukwa chiyani tiyenera kukhala ndi mtima ‘wodikira’ Yehova? (w03 8/15 24 ¶20)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Mika 4:1-10

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Sal. 83:18—Kuphunzitsa Choonadi​—Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Eks. 3:14—Kuphunzitsa Choonadi​—Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 132 ¶20-21.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 106

 • Zofunika Pampingo: (6 min.)

 • Yehova Amafuna Kuti Tikhale Opatsa (Miy. 3:27): (9 min.) Onetsani vidiyoyi.

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 10 ¶8-11 komanso tsamba 103 ndi 105 (kumanzere)

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 132 ndi Pemphero