Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  November 2016

November 21-27

MLALIKI 7-12

November 21-27
 • Nyimbo Na. 41 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Kumbukira Mlengi Wako Wamkulu Masiku a Unyamata Wako”: (10 min.)

  • Mlal. 12:1—Achinyamata ayenera kugwiritsa ntchito nthawi ndi mphamvu zawo potumikira Mulungu (w14 1/15 18 ndime 3; w14 1/15 22 ndime 1)

  • Mlal. 12:2-7—Achinyamata angachite zambiri chifukwa sakhala ndi mavuto amene anthu okalamba amakumana nawo (w08 11/15 23 ndime 2; w06 11/1 16 ndime 9)

  • Mlal. 12:13, 14—Kutumikira Yehova n’kumene kungakuthandizeni kukhala osangalala (w11 11/1 21 ndime 1-6)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Mlal. 10:1—Kodi “uchitsiru pang’ono” ungawononge bwanji mbiri ya munthu? (w06 11/1 16 ndime 5)

  • Mlal. 11:1—Kodi ‘kutumiza mkate wako pamadzi’ kumatanthauza chiyani? (w06 11/1 16 ndime 7)

  • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Mlal. 10:12-20; 11:1-10

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU