Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Apainiya akulalikira m’chinenero cha Chitsotsilu ku Chiapas m’dziko la Mexico

NDANDANDA YA UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU November 2016

Zitsanzo za Ulaliki

Zitsanzo za ulaliki wa Nsanja ya Olonda ndiponso mfundo ya m’Baibulo yokhudza ulosi umene ukukwaniritsidwa masiku ano. Gwiritsani ntchito zitsanzozi kuti mupange ulaliki wanuwanu.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Baibulo Limafotokoza Zimene Mkazi Wabwino Amachita

Kodi Yehova amafuna kuti mkazi wokwatiwa akhale ndi makhalidwe otani?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

“Mwamuna Wake Amadziwika Pazipata”

Mkazi wabwino amachititsa kuti mwamuna wake azilemekezedwa.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Muzisangalala Chifukwa Chogwira Ntchito Mwakhama

Tikhoza kumasangalala ndi ntchito yathu ngati timaiona moyenera.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Kodi Tingagwiritse Ntchito Bwanji Buku Lakuti Zimene Baibulo Limaphunzitsa?

Kodi tingagwiritse ntchito bwanji zinthu zimene zili m’buku la Zimene Baibulo limaphunzitsa tikamaphunzira ndi anthu?

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Kumbukira Mlengi Wako Wamkulu Masiku a Unyamata Wako”

M’chaputala 12 cha Mlaliki muli mawu andakatulo otilimbikitsa kutumikira Mulungu mwakhama tidakali achinyamata.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Achinyamata Musachedwe Kulowa ‘Pakhomo Lalikulu’

Kodi mungachite utumiki wa nthawi zonse kapena utumiki wina uliwonse?

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Msulami Ndi Chitsanzo Chabwino Kwambiri kwa Atumiki a Yehova

Kodi n’chiyani chinapangitsa kuti Msulami akhale chitsanzo chabwino kwa atumiki a Yehova?