• Nyimbo Na. 3 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Paulo Anali ndi ‘Munga M’thupi’”: (10 min.)

  • 2 Akor. 12:7​—Nthawi zonse Paulo ankalimbana ndi vuto linalake lomwe linali ngati munga m’thupi mwake (w08 6/15 3-4)

  • 2 Akor. 12:8, 9​—Ngakhale Paulo anachonderera Yehova kuti amuchotsere mungawo, Yehova sanauchotse (w06 12/15 24 ¶17-18)

  • 2 Akor. 12:10​—Paulo anakwanitsa kuchita utumiki wake chifukwa chodalira mzimu woyera wa Mulungu (w18.01 9 ¶8-9)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • 2 Akor. 12:2-4​—Kodi mawu akuti “kumwamba kwachitatu” komanso akuti ‘paradaiso’ ayenera kuti amatanthauza chiyani? (w18.12 8 ¶10-12)

  • 2 Akor. 13:12​—Kodi “kupsompsonana kwaubale” kunkaimira chiyani? (it-2 177)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) 2 Akor. 11:1-15 (th phunziro 5)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 38

 • Mukhoza Kumasangalalabe Ngakhale Muli ndi ‘Munga M’thupi’”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti “Maso a Anthu Akhungu Adzatsegulidwa” (Imapezeka pamene palembedwa kuti ZOCHITIKA PA MOYO WA ANTHU ENA) Dziwitsani abale ndi alongo kuti mabuku ndi zinthu zina zothandiza anthu amene ali ndi vuto losaona komanso zinthu zongomvetsera, zikupezeka m’zinenero 47. Ofalitsa alankhule ndi mtumiki wa mabuku kuti awaitanitsire zinthuzi. Limbikitsani onse kuti azikhala okonzeka kuthandiza anthu omwe ali ndi vutoli m’gawo la mpingo wanu.

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 36

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 119 ndi Pemphero