●○○ ULENDO WOYAMBA

Funso: Kodi tingadziwe bwanji zinthu zomwe zidzachitike m’tsogolo?

Lemba: Yes. 46:10

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi Mulungu amatilonjeza zotani zokhudza m’tsogolo komanso dziko lapansili?

○●○ ULENDO WOBWEREZA WOYAMBA

Funso: Kodi Mulungu amatilonjeza zotani zokhudza m’tsogolo komanso dziko lapansili?

Lemba: Sal. 37:29

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi tingatani kuti tidzaone nawo kukwaniritsidwa kwa malonjezo a m’Baibulo?

○○● ULENDO WOBWEREZA WACHIWIRI

Funso: Kodi tingatani kuti tidzaone nawo kukwaniritsidwa kwa malonjezo a m’Baibulo?

Lemba: Sal. 37:34

Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi Mulungu amafuna kuti tizichita chiyani pa moyo wathu?