CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Masomphenya Olimbitsa Chikhulupiriro”: (10 min.)

  • Maliko 9:1​—Yesu analonjeza atumwi ake ena kuti adzaona ulemerero umene adzakhale nawo mu Ufumu wake (w05 1/15 12 ¶9-10)

  • Maliko 9:2-6​—Pamene Yesu anasandulika, Petulo, Yakobo ndi Yohane anaona Yesu akuyankhulana ndi “Eliya” komanso “Mose” (w05 1/15 12 ¶11)

  • Maliko 9:7​—Yehova anatsimikizira anthuwa ndi mawu ake kuti Yesu ndi Mwana wake (“Mawu” mfundo zimene ndikuphunzira pa Maliko 9:7, nwtsty)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Maliko 10:6-9​—Kodi ndi mfundo iti yokhudza ukwati yomwe Yesu anaitchula palembali? (w08 2/15 30 ¶8)

  • Maliko 10:17, 18​—N’chifukwa chiyani Yesu anakana, munthu wina atamutchula kuti “Mphunzitsi Wabwino”? (“Mphunzitsi Wabwino” “Palibe wabwino koma Mulungu yekha” mfundo zimene ndikuphunzira pa Maliko 10:17, 18, nwtsty)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Maliko 9:1-13

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene.

 • Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.

 • Nkhani: (Osapitirira 6 min.) w04 5/15 30-31​—Mutu: Kodi Mawu a Yesu Opezeka pa Maliko 10:25 Amatanthauza Chiyani?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU