Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  May 2017

May15-21

YEREMIYA 39-43

May15-21
 • Nyimbo Na. 133 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Yehova Adzaweruza Aliyense Malinga ndi Ntchito Zake”: (10 min.)

  • Yer. 39:4-7—Zedekiya anakumana ndi mavuto chifukwa chosamvera Yehova (it-2-E 1228 ¶4)

  • Yer. 39:15-18—Yehova anayamikira Ebedi-meleki chifukwa chomukhulupirira (w12 5/1 31 ¶5)

  • Yer. 40:1-6—Yehova anasamalira Yeremiya yemwe anali mtumiki wake wokhulupirika (it-2-E 482)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Yer. 42:1-3; 43:2, 4—Kodi tikuphunzira chiyani kuchokera pa zimene Yohanani analakwitsa? (w03 5/1 10 ¶10)

  • Yer. 43:6, 7—Kodi zochitika zimene zafotokozedwa m’mavesiwa zili ndi ubwino wotani? (it-1-E 463 ¶4)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yer. 40:11–41:3

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Yes. 46:10—Kuphunzitsa Choonadi. Muuzeni nkhani imene mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Chiv. 12:7-9, 12—Kuphunzitsa Choonadi. Muuzeni nkhani imene mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bh 153 ¶19-20—Muitanireni munthuyo kumisonkhano.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU