Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YEREMIYA 35-38

Ebedi-meleki Ndi Chitsanzo Chabwino pa Nkhani ya Kulimba Mtima Komanso Kukoma Mtima

Ebedi-meleki Ndi Chitsanzo Chabwino pa Nkhani ya Kulimba Mtima Komanso Kukoma Mtima

Ebedi-meleki, yemwe anali nduna m’nyumba ya Mfumu Zedekiya, anasonyeza makhalidwe abwino

38:7-13

  • Iye anachita zinthu molimba mtima komanso mosazengereza pokafotokozera Mfumu Zedekiya zimene zinachitikira Yeremiya ndipo kenako anakamutulutsa m’chitsime

  • Anasonyeza kukoma mtima pomupatsa Yeremiya nsanza zoti aike m’khwapa kuti zingwe zisamuvulaze