Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  May 2017

May 8-14

YEREMIYA 35-38

May 8-14
 • Nyimbo Na. 33 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Ebedi-meleki Ndi Chitsanzo Chabwino pa Nkhani ya Kulimba Mtima Komanso Kukoma Mtima”: (10 min.)

  • Yer. 38:4-6—Zedekiya ankaopa anthu ndipo analola kuti anthuwo aponye Yeremiya m’chitsime chamatope kuti afe (it-2-E 1228 ¶3)

  • Yer. 38:7-10—Ebedi-meleki anachita zinthu molimba mtima komanso mosazengereza pofuna kupulumutsa Yeremiya (w12 5/1 31 ¶2-3)

  • Yer. 38:11-13—Ebedi-meleki anasonyeza kuti anali wokoma mtima (w12 5/1 31 ¶4)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Yer. 35:19—Kodi Arekabu anadalitsidwa chifukwa chiyani? (it-2-E 759)

  • Yer. 37:21—Kodi Yehova anathandiza bwanji Yeremiya, ndipo zimenezi zingatilimbikitse bwanji tikakumana ndi mavuto? (w98 1/15 18 ¶16-17; w95 8/1 5 ¶5-6)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yer. 36:27–37:2

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) wp17.3 chikuto—Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) wp17.3 chikuto—Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) jl phunziro 26

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 127

 • Kusamalira Malo Athu Olambirira: (15 min.) Nkhani ya mafunso ndi mayankho ndipo ikambidwe ndi mkulu. Pambuyo poonetsa vidiyo yakuti Kusamalira Malo Athu Olambirira komanso kukambirana mafunso, kambiranani mwachidule ndi m’bale amene ali m’komiti yoyang’anira Nyumba ya Ufumu. (Ngati palibe, funsani wogwirizanitsa ntchito za akulu. Ngati Nyumba ya Ufumuyo imagwiritsidwa ntchito ndi mpingo wanu wokha, funsani m’bale woyang’anira ntchito yosamalira Nyumba ya Ufumu.) Kodi ndi ntchito yosamalira Nyumba ya Ufumu yotani imene yachitika posachedwapa, ndipo pakonzedwa zotani kutsogoloku? Ngati pa mpingopo pali ena amene ali ndi luso, kapena amene akufuna kuphunzira lusolo kwa amene ali nalo kale, kodi ayenera kuchita chiyani? Kodi aliyense mumpingo angathandize bwanji kusamalira Nyumba ya Ufumu?

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 23 ¶15-29 komanso Mfundo Zofunika Kuziganizira patsamba 204

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 125 ndi Pemphero