• Nyimbo Na. 70 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Leka ‘Kufunafuna Zinthu Zazikulu’”: (10 min.)

  • Yer. 45:2,3—Baruki sankasangalala chifukwa cha maganizo olakwika amene anali nawo (jr 104-105 ¶4-6)

  • Yer. 45:4,5a—Yehova anathandiza Baruki mokoma mtima (jr 103 ¶2)

  • Yer. 45:5b—Baruki anapulumutsa moyo wake chifukwa choika maganizo ake pa zinthu zofunika kwambiri (w16.07 8 ¶6)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Yer. 48:13—N’chifukwa chiyani ‘Amowabu anachita manyazi ndi Kemosi’? (it-1-E 430)

  • Yer. 48:42—Kodi kuganizira za chiweruzo chimene Yehova anapereka kwa Amowabu kungalimbitse bwanji chikhulupiriro chathu? (it-2-E 422 ¶2)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yer. 47:1-7

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) hf—Muuzeni nkhani imene mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) hf—Muuzeni nkhani imene mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) lv 199 ¶9-10—Mwachidule sonyezani wophunzira mmene angafufuzire malangizo pa nkhani yokhudza vuto linalake limene akukumana nalo.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU