Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  May 2017

 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YEREMIYA 32-34

Chizindikiro Chosonyeza Kuti Aisiraeli Adzabwerera Kwawo

Chizindikiro Chosonyeza Kuti Aisiraeli Adzabwerera Kwawo
ONANI
Kukula kwa Zilembo
Chithunzi

32:9-14

  • Yeremiya anatsatira malamulo ofunika pogula munda.

33:10, 11

  • Yehova anasonyeza kuti ndi wabwino polonjeza anthu ake omwe anali ku ukapolo kuti akamvera malangizo ake, adzawakhululukira ndipo adzabwerera ku Isiraeli.

Kodi Yehova wasonyeza bwanji kuti ndi wabwino kwa inuyo?