Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  May 2016

May 9-15

MASALIMO 1-10

May 9-15
 • Nyimbo 99 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Tizilemekeza Yesu Kuti Tikhale Pamtendere ndi Yehova”: (10 min.)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Sal. 2:7—Kodi “lamulo la Yehova” n’chiyani? (w06 5/15 17 ndime 6)

  • Sal. 4:4—Kodi mawu akuti “Lankhulani mumtima mwanu, muli pabedi panu, ndipo mukhale chete” amatanthauza chiyani? (w11 5/15 31 ndime 18)

  • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Salimo 8:1–9:10

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) wp16.3 Nkhani ya pachikuto—Werengani lemba pogwiritsa ntchito foni kapena chipangizo china chamakono.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) wp16.3 Nkhani ya pachikuto—Chitani chitsanzo chosonyeza mwininyumba akukana kumuwerengera lemba mu Baibulo la Dziko Latsopano. Kenako gwiritsani ntchito Laibulale ya JW kuti mumusonyeze mmene lembalo analimasulira mu Mabaibulo ena.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bh 12 ndime 12-13—Limbikitsani wophunzirayo kuti apange dawunilodi Laibulale ya JW mufoni yake.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 138

 • Uzilemekeza Nyumba ya Yehova: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo ya pa jw.org yakuti Khalani Bwenzi la Yehova—Uzilemekeza Nyumba ya Yehova (Pitani pamene palembedwa kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ANA.) Kenako itanani ana ang’onoang’ono kuti abwere kupulatifomu ndipo muwafunse zomwe aphunzira mu vidiyoyo.

 • Dzina la Mulungu M’Malemba Achiheberi: (10 min.) Nkhani yochokera mu Kabuku Kothandiza Kuphunzira Baibulo mutu 1.

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) cl mutu 30 ndime 1-9

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 11 ndi Pemphero