Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  May 2016

 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MASALIMO 19-25

Zimene Maulosi Ananena Zokhudza Mesiya

Zimene Maulosi Ananena Zokhudza Mesiya

LEMBA

ULOSI

KUKWANIRITSIDWA KWAKE

Salimo 22:1

Anaoneka ngati wasiyidwa ndi Mulungu

Mateyu 27:46; Maliko 15:34

Salimo 22:7, 8

Ananyozedwa ali pamtengo wozunzikirapo

Mateyu 27:39-43

Salimo 22:16

Anamukhomerera pamtengo

Mateyu 27:31; Maliko 15:25; Yohane 20:25

Salimo 22:18

Anachita mayere pazovala zake

Mateyu 27:35

Salimo 22:22

Anatsogolera pa ntchito yolalikira za dzina la Yehova

Yohane 17:6