Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  May 2016

May 23-29

MASALIMO 19-25

May 23-29
 • Nyimbo Na. 116 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Zimene Maulosi Ananena Zokhudza Mesiya”: (10 min.)

  • Sal. 22:1—Mesiya adzaoneka ngati wasiyidwa ndi Mulungu. (w11 8/15 15 ndime 16)

  • Sal. 22:7, 8—Mesiya adzanyozedwa. (w11 8/15 15 ndime 13)

  • Sal. 22:18—Anthu adzachita mayere pa zovala za Mesiya. (w11 8/15 15 ndime 14)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Sal. 19:14—Kodi tingaphunzire chiyani pavesili? (w06 5/15 19 ndime 7)

  • Sal. 23:1, 2—N’chifukwa chiyani tinganene kuti Yehova ndi mbusa wachikondi? (w02 9/15 32 ndime 1-2)

  • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Salimo 25:1-22

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) bh—Werengani lemba pogwiritsa ntchito foni kapena chipangizo china chamakono.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) bh—Gwiritsani ntchito kachizindikiro kofufuzira ka pa JW Library kuti mupeze vesi limene likuyankha funso la mwininyumba.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bh 129-130 ndime 11-12—Sonyezani mwachidule wophunzirayo mmene angagwiritsire ntchito Laibulale ya JW pokonzekera phunziro la Baibulo pafoni kapena chipangizo china.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU