Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu  |  May 2016

May 16-22

MASALIMO 11-18

May 16-22
 • Nyimbo Na. 106 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Ndani Angakhale Mlendo M’chihema cha Yehova?”: (10 min.)

  • Sal. 15:1, 2—Tizilankhula zoona mumtima mwathu (w03 8/1 14 ndime 18; w89 9/15 27 ¶1)

  • Sal. 15:3—Tiyenera kulankhula zinthu zabwino (w89 10/15 12 ndime 10-11; w89 9/15 27 ndime 3-4; w14 2/15 23, ndime 10-11)

  • Sal. 15:4, 5—Tizikhala okhulupirika nthawi zonse (w06 5/15 19 ndime 1; w89 9/15 29-30; it-1-E 1211 ndime 3)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Sal. 11:3—Kodi vesili likutanthauza chiyani? (w06 5/15 18 ndime 2; w05 5/15 32 ndime 2)

  • Sal. 16:10—Kodi ulosiwu unakwaniritsidwa bwanji pa Yesu Khristu? (w11 8/15 16 ndime 19; w05 5/1 14 ndime 9)

  • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Sal. 18:1-19

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) wp16.3 16—Werengani lemba pogwiritsa ntchito foni kapena chipangizo china chamakono.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) wp16.3 16—Tsegulani Laibulale ya JW ndi kuwerenga malemba n’cholinga choti mwininyumba amve malembawo m’chinenero chake.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bh 100-101 ndime 10-11—Sonyezani mwachidule wophunzirayo mmene angagwiritsire ntchito Laibulale ya JW pofufuza yankho la funso limene wafunsa.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU