Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Banja likuphunzira Baibulo pogwiritsa ntchito tabuleti

NDANDANDA YA UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU May 2016

Zitsanzo za Ulaliki

Mfundo zokuthandizani pogawira Nsanja ya Olonda ndi buku lakuti Baibulo Limaphunzitsa Chiyani. Gwiritsani ntchito zitsanzozi kuti mupange ulaliki wanuwanu.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova Amasangalala Tikamapempherera Ena

Mulungu anauza Yobu kuti apempherere anzake atatu. Kodi Yobu anadalitsidwa bwanji chifukwa cha chikhulupiriro komanso kupirira? (Yobu 38-42)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Kodi Mumagwiritsa Ntchito Laibulale ya JW?

Kodi laibulaleyi mungaipeze bwanji? Kodi ingakuthandizeni bwanji pamisonkhano ya mpingo ndi mu utumiki?

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Tizilemekeza Yesu Kuti Tikhale Pamtendere ndi Yehova

Kodi anthu a mitundu yosiyanasiyana amauona bwanji ulamuliro wa Yesu? N’chifukwa chiyani tiyenera kulemekeza Mfumu yosankhidwa ndi Mulungu? (Salimo 2)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Ndani Angakhale Mlendo M’chihema cha Yehova?

Salimo 15 limafotokoza zimene Yehova amafuna kuti anzake azichita.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Mmene Tingagwiritsire Ntchito Laibulale ya JW

Mmene tingagwiritsire ntchito laibulale ya jw pophunzira, kumisonkhano ndiponso mu utumiki.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Zimene Maulosi Ananena Zokhudza Mesiya

Werengani nkhaniyi kuti muone mmene maulosi a mu Salimo 22 anakwaniritsidwira pa Yesu.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Tizidalira Yehova Kuti Tikhale Olimba Mtima

N’chiyani chingatithandize kuti tikhale olimba mtima ngati Davide? (Salimo 27)