CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 18

  • Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki​—Muzilemba Makalata Abwino”: (8 min.) Nkhani yokambirana.

  • Ntchito Yoitanira Anthu ku Chikumbutso Idzayamba pa 23 March: (7 min.) Nkhani yokambidwa ndi woyang’anira utumiki. Perekani kapepala koitanira anthu ku Chikumbutso kwa aliyense n’kukambirana mfundo zake. Onerani ndi kukambirana vidiyo ya zimene tinganene pogawira kapepala koitanira anthu ku Chikumbutso. Fotokozani zimene mpingo wanu wakonza kuti mudzathe kugawira timapepalati kwa anthu onse a m’gawo lanu.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 30

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 5 ndi Pemphero