Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Ku South Africa, akugwiritsa ntchito vidiyo pophunzira ndi munthu

NDANDANDA YA UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU March 2019

Zimene Tinganene

Zitsanzo za ulaliki zotithandiza kumvetsa cholinga chomwe Mulungu analengera anthu.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Mmene Tingasonyezere Chikondi Chachikhristu

Kodi tingasonyeze chikondi chachikhristu ngati munthu wina atatilakwira?

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Muzidalira Yehova Kuti Akulimbikitseni Komanso Kukuthandizani Kupirira

Njira imodzi imene Yehova amatilimbikitsira komanso kutithandiza kupirira ndi kudzera m’Mawu ake.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kodi Ndinu Munthu Wakuthupi Kapena Munthu Wauzimu?

Tonse tiyenera kupitirizabe kukula mwauzimu n’kufika pomaona zinthu mmene Yehova amazionera.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki​​—Muzilemba Makalata Abwino

Kodi tiyenera kumakumbukira chiyani tikamalembera kalata munthu amene sitikumudziwa?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Kalata Yachitsanzo

Mukhoza kusintha zina ndi zina pakalata yachitsanzoyi kuti igwirizane ndi cholinga chanu, chikhalidwe komanso mmene zinthu zilili kwanuko.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Chofufumitsa Chaching’ono Chimafufumitsa Mtanda Wonse”

N’chifukwa chiyani tinganene kuti kuchotsa munthu kumasonyeza chikondi?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Muzigwiritsa Ntchito Mavidiyo Pophunzira ndi Anthu

Kodi mumagwiritsa ntchito mavidiyo mukamaphunzira Baibulo ndi anthu?