CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Aliyense Wofuna Kukhala Wamkulu Pakati Panu Ayenera Kukhala Mtumiki Wanu”: (10 min.)

  • Mat. 20:3​—Alembi ndi Afarisi onyada ankasangalala akamalemekezedwa komanso kupatsidwa ulemu “pamsika” (Zithunzi ndi mavidiyo za “pamsika” pa Mat. 20:3, nwtsty)

  • Mat. 20:20, 21​—Atumwi awiri anapempha kuti apatsidwe udindo komanso malo aulemu (Mfundo zimene ndikuphunzira za “mkazi wa Zebedayo,” “mmodzi kudzanja lanu lamanja, wina kumanzere kwanu” pa Mat. 20:20, 21, nwtsty)

  • Mat. 20:25-28​—Yesu anafotokoza kuti otsatira ake ayenera kukhala odzichepetsa (Mfundo zimene ndikuphunzira za “mtumiki” pa Mat. 20:26, nwtsty)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Mat. 21:9​—Kodi anthu amene ankafuula kuti, “M’pulumutseni Mwana wa Davide!” ankatanthauza chiyani? (Mfundo zimene ndikuphunzira za “M’pulumutseni,” “Mwana wa Davide” pa Mat. 21:9, nwtsty)

  • Mat. 21:18, 19​—Kodi n’chifukwa chiyani Yesu anachititsa kuti mtengo wa mkuyu ufote? (jy 244 ¶4-6)

  • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Mat. 20:1-19

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 99

 • Zofunika Pampingo: (5 min.)

 • Zimene Gulu Lathu Lachita: (10 min.) Onetsani vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya March.

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 15 ¶1-8

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 53 ndi Pemphero