Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

March 20-26

YEREMIYA 8-11

March 20-26
 • Nyimbo Na. 117 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Anthu Akamatsogoleredwa ndi Yehova Zinthu Zimawayendera Bwino”: (10 min.)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Yer. 9:24—Kodi ndi kunyada ndiponso kudzitamanda kotani komwe ndi kwabwino? (w13 1/15 20 ¶16)

  • Yer. 11:10—N’chifukwa chiyani Yeremiya anaphatikiza ufumu wakumpoto wa mafuko 10 mu uthenga wake ngakhale kuti Samariya anali atawonongedwa kale mu 740 B.C.E.? (w07 3/15 9 ¶2)

  • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yer. 11:6-16

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

 • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Kapepala koitanira anthu ku Chikumbutso ndiponso wp17.2 chikuto—Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Kapepala koitanira anthu ku Chikumbutso wp17.2 chikuto—Muuzeni zimene mudzakambirane ulendo wotsatira.

 • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) ld tsamba 4-5 (Wofalitsa angasankhe zithunzi zomwe akufuna kukambirana.)—Muitanireni ku Chikumbutso.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU