Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

March 7-13

ESITERE 6-10

March 7-13
 • Nyimbo Na. 131 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Esitere Anasonyeza Kuti Sanali Wodzikonda”: (10 min.)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Esitere 8:1, 2—Kodi ulosi umene Yakobo ananena atatsala pang’ono kufa wakuti ‘madzulo Benjamini adzagawa zimene wafunkha,’ unakwaniritsidwa bwanji? (ia 142, bokosi)

  • Esitere 9:10, 15, 16—N’chifukwa chiyani Ayuda sanalande zofunkha ngakhale kuti lamulo linawalola kuchita zimenezi? (w06 3/1 11 ndime 4)

  • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: Esitere 8:1-9 (Osapitirira 4 min.)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 118

 • Tidzalandire Bwino Alendo”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Pemphani ofalitsa kuti afotokoze zinthu zabwino zimene zinachitika chifukwa cholandira bwino alendo pa Chikumbutso cha chaka chatha. Chitani chitsanzo chosonyeza zinthu zabwino zimene zinachitika.

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: cl mutu 27 ndime 1-9 (30 min.)

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 147 ndi Pemphero