Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

March 28–April 3

YOBU 11-15

March 28–April 3
 • Nyimbo Na. 111 ndi Pemphero

 • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

 • Yobu Sankakayikira Kuti Akufa Adzauka”: (10 min.)

 • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

  • Yobu 12:12—N’chifukwa chiyani tinganene kuti Akhristu achikulire angathandize Akhristu achinyamata? (g99 8/8 11, bokosi)

  • Yobu 15:27—Kodi Elifazi ankatanthauza chiyani pamene ananena kuti nkhope ya Yobu “yaphimbika ndi mafuta”? (it-1-E 802 ndime 4)

  • Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?

 • Kuwerenga Baibulo: Yobu 14:1-22 (Osapitirira 4 min.)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

 • Nyimbo Na. 134

 • Zofunika pampingo: (5 min.)

 • Imfa ya Yesu Inathandiza Kuti Akufa Adzaukitsidwe”: (10 min.) Nkhani yokambirana. Pomaliza onetsani vidiyo imene inaonetsedwa pa Msonkhano Wachigawo wa 2014 wakuti, “Pitirizani Kufunafuna Ufumu wa Mulungu Choyamba.”

 • Phunziro la Baibulo la Mpingo: cl mutu 28 ndime 1-9 (30 min.)

 • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

 • Nyimbo Na. 33 ndi Pemphero